Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Akorinto 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndingakhale ndipereka cuma cangaconsekudyetsa osauka, ndipo ndingakhalendipereka thupi langa alitenthe m'moto, koma ndiribe cikondi, sindipindula kanthu ai.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 13

Onani 1 Akorinto 13:3 nkhani