Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 17:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Gawo la pfuko la Manase ndi ili: pakuti anali woyamba wa Yosefe. Makiri mwana woyamba wa Manase, atate wa Gileadi, popeza ndiye munthu wa nkhondo, anakhala nayo Gileadi ndi Basana.

2. Ndipo maere anagwera ana ena otsala a Manase monga mwa mabanja ao; ana a Abiezere ndi ana a Heleki, ndi ana a Asiriyeli, ndi ana a Sekemu ndi ana a Hefere, ndi ana a Semida; awa ndi ana amuna a Manase mwana wa Yosefe, monga mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 17