Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 17:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Tselofekadi, mwana wa Hefere, mwana wa Gileadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, analibe ana amuna koma ana akazi ndiwo; ndipo maina a ana ace akazi ndiwo: Mala, ndi Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 17

Onani Yoswa 17:3 nkhani