Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 17:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo maere anagwera ana ena otsala a Manase monga mwa mabanja ao; ana a Abiezere ndi ana a Heleki, ndi ana a Asiriyeli, ndi ana a Sekemu ndi ana a Hefere, ndi ana a Semida; awa ndi ana amuna a Manase mwana wa Yosefe, monga mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 17

Onani Yoswa 17:2 nkhani