Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inenso ndidzasankha zodzinyenga nazo, ndipo ndidzatengera mantha ao pa iwo; pakuti pamene ndinaitana, panalibe woyankha; pamene ndinalankhula, iwo sanamva konse; koma anacita coipa m'maso mwanga, ndi kusankha cimene ndisanakondwere naco.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:4 nkhani