Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wakupha ng'ombe alingana ndi wakupha munthu; iye wapereka nsembe ya mwana wa nkhosa alingana ndi wotyola khosi la garu; wothira nsembe yaufa akunga wothira mwazi wa nkhumba; wofukiza conunkhira akunga wodalitsa fano; inde iwo asankha njira zao zao, ndipo moyo wao ukondwerera m'zonyansa zao;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:3 nkhani