Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudzi wonse uthawa m'phokoso la apakavalo ndi amauta; adzalowa m'nkhalango, adzakwera pamiyala; midzi yonse idzasiyidwa, ndipo simudzakhala munthu m'menemo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:29 nkhani