Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanga iwe, udzacita ciani pamene udzafunkhidwa? Ngakhale udzibveka ndi zofiira, ngakhale udzibveka ndi zokometsera zagolidi, ngakhale udzikuzira maso ako ndi kupaka, udzikometsera pacabe; mabwenzi adzakunyoza adzafuna moyo wako.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:30 nkhani