Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 33:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, cifundo cace ncosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33

Onani Yeremiya 33:11 nkhani