Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 33:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu atero: M'malo muno, muli bwinja, mopanda munthu ndi nyama, m'midzi yace yonse, mudzakhalanso mokhalamo abusa ogonetsa zoweta zao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33

Onani Yeremiya 33:12 nkhani