Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 33:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova: M'malo muno, m'mene muti, Ndi bwinja, mopanda munthu, mopanda nyama, m'midzi ya Yuda, m'makwalala a Yerusalemu, amene ali bwinja, opanda munthu, opanda wokhalamo, opanda nyama,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33

Onani Yeremiya 33:10 nkhani