Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala, pamene adzati kwa iwe, Titurukire kuti? pamenepo uziti, Atero Yehova: Amene a kuimfa, anke kuimfa; amene a kulupanga, anke kulupanga; amene a kunjala, anke kunjala; ndi amene a kunsinga, anke kunsinga.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 15

Onani Yeremiya 15:2 nkhani