Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatuma amithenga kwa Balamu mwana wa Beori, ku Petori, wokhala kumtsinje, wa dziko la anthu a mtundu wace, kuti amuitane, ndi kuti, Taonani, anaturuka anthu m'dziko la Aigupto; taonani, aphimba nkhope ya dziko, nakhala popenyana ndi ine.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:5 nkhani