Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, idzatu, nunditembererere anthu awa; popeza andiposa mphamvu; kapena ndidzawalaka, kuti tiwakanthe, ndi kuti ndiwapitikitse m'dziko; pakuti ndidziwa kuti iye amene umdalitsa adalitsika, ndi iye amene umtemberera atemberereka.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:6 nkhani