Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amitundu ambiri adzamuka, nadzati, Tiyeni, tikwere ku phiri la Yehova, ndi ku nyumba ya Mulungu wa Yakobo; kuti Iye atiphunzitse njira zace, ndipo tidzayenda m'mabande ace; pakuti ku Ziyoni kudzaturuka cilamulo, ndi ku Yerusalemu mau a Yehova.

Werengani mutu wathunthu Mika 4

Onani Mika 4:2 nkhani