Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye adzaweruza mwa mitundu yambiri ya anthu, nadzadzudzula amitundu amphamvu ali kutali; ndipo iwo adzasula malupanga ao akhale makasu, ndi mikondo yao ikhale mazenga, mtundu wa anthu sudzasamulira mtundu unzace lupanga, kapena kuphunziranso nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Mika 4

Onani Mika 4:3 nkhani