Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Mika 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kudzacitika masiku otsiriza, kuti phiri la nyumba ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa mapiri, nilidzakuzika pamwamba pa zitunda; ndi mitundu ya anthu idzayendako.

Werengani mutu wathunthu Mika 4

Onani Mika 4:1 nkhani