Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 17:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndiwo moyo wa: nyama zonse, mwazi wace ndiwo moyo wace; cifukwa cace ndinanena kwa ana a Israyeli, Musamadya mwazi wa nyama iri yonse; pakuti moyo wa nyama yonse ndi mwazi wace; ali yense akaudya adzasadzidwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 17

Onani Levitiko 17:14 nkhani