Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo musakhale munthu m'cihema cokomanako pakulowa iye kucita cotetezera m'malo opatulika, kufikira aturuka, atacita cotetezera yekha, ndi mbumba yace, ndi msonkhano wonse wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:17 nkhani