Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo aturukire guwa la nsembe lokhala pamaso pa Yehova ndi kulicitira cotetezera; natengeko mwazi wa ng'ombeyo, ndi mwazi wa mbuziyo, ndi kuupaka pa nyanga za guwa la nsembe pozungulira.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:18 nkhani