Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 12:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akabala mwana wamkazi, akhale wodetsedwa masabata awiri, monga umo amakhala padera; ndipo adzakhala m'mwazi wa kumyeretsa kwace masiku makumi asanu ndi limodzi kudza asanu ndi limodzi.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 12

Onani Levitiko 12:5 nkhani