Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 12:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akhale m'mwazi wa kumyeretsa kwace masiku makumi atatu kudza atatu; asakhudze kanthu kopatulika, kapena kulowa m'malo opatulika, kufikira adakwanira masiku a kumyeretsa kwace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 12

Onani Levitiko 12:4 nkhani