Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atakwanira masiku a kumyeretsa kwace pa mwana wamwamuna, kapena mwana wamkazi, adze naye mwana wa nkhosa wa caka cimodzi ikhale nsembe yopsereza, ndi bunda, kapena njiwa zikhale nsembe yaucimo, ku khomo la cihema cokomanako, kwa wansembe;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 12

Onani Levitiko 12:6 nkhani