Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 36:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Esau anatenga akazi ace, ndi ana ace amuna, ndi ana ace akazi, ndi anthu onse a m'banja mwace, ndi ng'ombe zace, ndi zoweta zace, ndi zonse anali nazo anasonkhanitsa m'dziko la Kanani; ndipo ananka ku dziko losiyana patari ndi Yakobo mphwace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 36

Onani Genesis 36:6 nkhani