Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 36:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cuma cao cinali cambiri cotero kuti sanakhoza kukhala pamodzi; ndipo dziko lokhalamo iwo silinakhoza kuwakwanira cifukwa ca ng'ombe zao.

Werengani mutu wathunthu Genesis 36

Onani Genesis 36:7 nkhani