Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 36:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Oholibama anabala Jeusi, ndi Jalamu, ndi Kora; amenewa ndi ana amuna a Esau, amene anambadwira m'dziko la Kanani.

Werengani mutu wathunthu Genesis 36

Onani Genesis 36:5 nkhani