Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzamdalitsa iye, ndiponso ndidzakupatsa iwe mwana wamwamuna wobadwa mwa iye, inde, ndidzamdalitsa iye, ndipo adzakhala amace a mitundu, mafumu a anthu adzaturuka mwa iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:16 nkhani