Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anati kwa Abrahamu, Koma Sarai mkazi wako, usamcha dzina lace Sarai, koma dzina lace ndi Sara.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:15 nkhani