Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:14-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. kodi tidzabwereza kuphwanya malamulo anu, ndi kukwatana nayo mitundu ya anthu ocita zonyansa izi? Simudzakwiya nafe kodi mpaka mwatitha, ndi kuti pasakhale otsala kapena akupulumuka?

15. Yehova Mulungu wa Israyeli, Inu ndinu wolungama, popeza tinatsala opulumuka monga lero lino; taonani, tiri pamaso panu m'kuparamula kwathu; pakuti palibe wakuima pamaso panu cifukwa ca ici.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9