Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitatigwera zonsezi cifukwa ca nchito zathu zoipa ndi kuparamula kwathu kwakukuru; popeza inu Mulungu wathu mwatilanga moticepsera mphulupulu zathu, ndi ku tipatsa cipulumutso cotere;

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:13 nkhani