Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova Mulungu wa Israyeli, Inu ndinu wolungama, popeza tinatsala opulumuka monga lero lino; taonani, tiri pamaso panu m'kuparamula kwathu; pakuti palibe wakuima pamaso panu cifukwa ca ici.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:15 nkhani