Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono, musamapereka ana anu akazi kwa ana ao amuna, kapena kutengera ana anu amuna ana ao akazi, kapena kufuna mtendere wao ndi kukoma kwao nthwawi yonse, kuti mukhale olimba, ndi kudya zokoma za m'dziko, ndi kulisiyira ana anu colowa ca ku nthawi yonse.

Werengani mutu wathunthu Ezara 9

Onani Ezara 9:12 nkhani