Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti Ayuda anasonkhana pamodzi m'midzi mwao, m'maiko onse a mfumu Ahaswero, kuwathira manja ofuna kuwacitira coipa, ndipo palibe munthu analimbika pamaso pao; popeza kuopsa kwao kudawagwera mitundu yonse ya anthu.

Werengani mutu wathunthu Estere 9

Onani Estere 9:2 nkhani