Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwezi wakhumi ndi ciwiri tsono, ndiwo mwezi wa Adara, tsiku lace lakhumi ndi citatu, mau a mfumu ndi lamulo lace ali pafupi kucitika, tsikuli adani a Ayuda anayesa kuwacitira ufumu, koma cinasinthika; popeza Ayuda anacitira ufumu iwo odana nao;

Werengani mutu wathunthu Estere 9

Onani Estere 9:1 nkhani