Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 9:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akalonga onse a maikowo, ndi akazembe, ndi ziwanga, ndi iwo ocita nchito ya mfumu, anathandiza Ayuda; popeza kuopsa kwa Moredekai kudawagwera.

Werengani mutu wathunthu Estere 9

Onani Estere 9:3 nkhani