Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwezi woyamba, tsiku lace lakhumi ndi cinai madzulo ace, muzidya mkate wopanda cotupitsa, kufikira tsiku la makumi awiri mphambu limodzi la mwezi, madzulo ace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 12

Onani Eksodo 12:18 nkhani