Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 10:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dzombe linakwera pa dziko lonse la Aigupto, ndipo linatera pakati pa malire onse a Aigupto, lambirimbiri; lisanafike ili panalibe dzombe lotere longa ili, ndipo litapita ili sipadzakhalanso lotere.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 10

Onani Eksodo 10:14 nkhani