Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 10:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti linakuta nkhope ya dziko lonse kuti dziko linada; ndipo linadya zitsamba zonse za m'dziko, ndi zipatso zonse za mitengo zimene matalala adazisiya; ndipo sipanatsala cabiriwiri ciri conse, pamitengo kapena pa zitsamba za kuthengo, m'dziko lonse la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 10

Onani Eksodo 10:15 nkhani