Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 24:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo mwamuna woyamba anamcotsayo sangathe kumtenganso akhale mkazi wace, atadetsedwa iye; pakuti ici ndi conyansa pamaso pa Yehova; ndipo usamacimwitsa dziko, limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale colandira canu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:4 nkhani