Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 24:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akatenga mkazi watsopano, asaturuke nayo nkhondo, kapena asamcititse kanthu kali konse; akhale waufulu ku nyumba yace caka cimodzi, nakondweretse mkazi adamtengayo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:5 nkhani