Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku asanu ndi awiri mucitire Yehova Mulungu wanu madyerero m'malo amene Yehova adzasankha; popeza Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani m'zipatso zanu zonse, ndi m'nchito zonse za manja anu; nimukondwere monsemo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:15 nkhani