Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amuna onse azioneka pamaso pa Yehova Mulungu wanu m'malo amene iye adzasankha, katatu m'caka; pa madyerero a mkate wopanda cotupitsa, pa madyerero a masabata, ndi pa madyerero a misasa; ndipo asaoneke pamaso pa Yehova opanda kanthu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:16 nkhani