Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nimukondwere m'madyerero mwanu, inu, ndi ana anu amuna, ndi ana anu akazi, ndi anchito anu amuna, ndi anchito anu akazi, ndi Mlevi, ndi mlendo, ndi mwana wamasiye, ndi mkazi wamasiye okhala m'mudzi mwanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:14 nkhani