Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo padasandulika pa nkhope pace pa mfumu, ndi maganizo ace anamsautsa, ndi mfundo za m'cuuno mwace zinaguruka, ndi maondo ace anaombana.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:6 nkhani