Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nipfuulitsa mfumu abwere nao openda, Akasidi, ndi alauli, Mfumu inalankhula, niti kwa anzeru a ku Babulo, Ali yense amene adzawerenga lemba ili, nadzandifotokozera kumasulira kwace, adzabvekedwa cibakuwa, ndi unyolo wagolidi m'khosi mwace, nadzakhala wolamulira wacitatu m'ufumuwu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:7 nkhani