Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoabu ananena ndi mfumu, Yehova Mulungu wanu aonjezere kwa anthu monga ali kuwacurukitsa makumi khumi, ndi maso a mbuye wanga mfumu acione; koma mbuye wanga mfumu alikukondwera bwanji ndi cinthu ici?

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:3 nkhani