Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inanena ndi Yoabu kazembe wa khamu, amene anali naye, Kayendere tsopano mafuko onse a Israyeli, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba, nuwerenge anthuwo, kuti ndidziwe kucuruka kwao kwa anthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:2 nkhani