Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Yehova anatumiza mliri pa Israyeli kuyambira m'mawa kufikira nthawi yoikika; ndipo anafapo anthu zikwi makumi asanu ndi awiri kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:15 nkhani