Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena ndi Gadi, Ndipsinjika mtima kwambiri, tigwe m'dzanja la Yehova; pakuti zifundo zace nzazikuru; koma tisagwe m'dzanja la munthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:14 nkhani