Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 2:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yoabu ndi Abisai anampitikitsa Abineri; ndipo dzuwa linawalowera pofika ku citunda ca Ama, cakuno ca Giya, pa njira ya ku cipululu ca Gibeoni.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:24 nkhani